@NatureMw155

Ngati uvomereza kuti iyi ndi voice ya maremu Grace chinga paseni 10000 likes❀

@MatridawaBanda

Amene tayamba kuonera mmawa mpaka pano tikumanene paselipa tili ndizokambiranaπŸ”₯πŸ”₯πŸ’ƒ

@clemjonesngambi

Heavenly father i pray that you keep the person reading this alive, safe, healthy, and financially blessed Amen

@DavieKhumvahe

Basi ndavomereza kuti uyu ndiwoimba sizokakamiza. Ndiangati tivomereza like my comment 😊

@tamandanieunicekatunga7386

Well composed..... zabwino kumayamikiraπŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ₯³πŸ₯³πŸ₯³

@NyifwayaoMwale

Am not tired of watching this video, this is powerful.Zambians let's gather here πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰

@BillyGuanChifika-p2k

You won my heart with Mseri, convinced me you're a great artist with Thamanga and now Mmodzi made me believe Grace is still ministering in you❀️

@Rodger-Kadammanja34lw5s

How can I like this song a thousand times? This song ma Guy is something else. Kiss πŸ’‹ this comment so that I can keep on coming here for the Melody and Soothing voice of Miracle

@simkaymusic

Ndi angat amene tikufila ngat grace chingat is back

@PatrickKanthenga-q3c

Spiritually I am okey plus this hit wawooo!!! Thank you miracle yesu mmodzi uja is with me through this great song

@KeysTosuccess-b2y

Iwe ukuwerengawe, nsanje sipindula. Mwanayu amatha kuyimba❀

@EllenNamate-r9c

Iyi mwapha adona ,zabwino kumayamikira ndithuπŸ₯³β™₯️

@brightcharlie2396

Amene taonera crues 5 ukucheza nd joab tikumane pano kut uyu zomwe analankhula zili mu nyimbo iyi

@binletkamanga8540

From Nigeria to support you Miracle ChingaπŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰

@BLESS-T

Sindinamukaikirepo Miracle kumbali yamaimbidwe. Mtsikana uyu amatha. Legacy yamai ndi iyeyu.πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯

@WlisonMalengaMandera

God loves us no matter what still loving us.....big sister your a preacher send by Power of God.....mutisutha kwambiri ndi nyimbo zanu never give up until we meet Jesus in heaven

@AginessMwenyekonde-k7y

Iyiyi ndiye ndiyeniyeni amwene bwenzi ndi Yesu sawona nyengo ndithu  Amen

@CarthyMatenje

Verse 1 ikukamba za nyengo yanga eeeeeeπŸ™ŒπŸ™Œbwenzi koma yesu indeed

@PattieMkombezi

100% talented .... grace chinga legacy

@OwenKambwiri-c6i

Miracle chinga you finish me with this songπŸŽ‰πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚